Salimo 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mudzawononga olankhula bodza.+Munthu wokhetsa magazi+ ndi wachinyengo,+ Yehova amaipidwa naye. Miyambo 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kuopa Yehova kudzawonjezera masiku,+ koma zaka za anthu oipa zidzafupikitsidwa.+ Mlaliki 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usakhale woipa mopitirira muyezo,+ komanso usakhale wopusa.+ Uferenji mwamsanga?+ Mateyu 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho iye anaponya ndalama zasiliva zija m’kachisi n’kuchoka, ndipo anakadzimangirira.+