Salimo 55:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipa kumanda.+Ndipo anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso anthu achinyengo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+Koma ine ndidzakhulupirira inu.+ Mlaliki 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usakhale woipa mopitirira muyezo,+ komanso usakhale wopusa.+ Uferenji mwamsanga?+
23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipa kumanda.+Ndipo anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso anthu achinyengo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+Koma ine ndidzakhulupirira inu.+