Salimo 56:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndimadalira Mulungu. Sindidzaopa.+Kodi munthu wochokera kufumbi angandichite chiyani?+ Salimo 115:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu oopa Yehova, khulupirirani Yehova.+Iye ndiye thandizo lanu ndi chishango chanu.+