Salimo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:“Kulibe Yehova.”+Anthu oterewa amachita zoipa,+ ndipo amachita zinthu zonyansa.Palibe amene akuchita zabwino.+ Salimo 75:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu opusa ndinawauza kuti: “Musakhale opusa,”+Ndipo oipa ndinawauza kuti: “Musakweze nyanga.*+ Miyambo 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu opusa akapalamula mlandu amangoseka,+ koma pakati pa anthu owongoka mtima pali mgwirizano.+
14 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:“Kulibe Yehova.”+Anthu oterewa amachita zoipa,+ ndipo amachita zinthu zonyansa.Palibe amene akuchita zabwino.+