Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 10:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Kwa wopusa, kusonyeza khalidwe lotayirira kuli ngati masewera,+ koma nzeru zimakhala ndi munthu wozindikira.+

  • Miyambo 30:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Nayi njira ya mkazi wachigololo: Iye amadya n’kupukuta pakamwa pake ndipo amanena kuti: “Sindinachite cholakwa chilichonse.”+

  • Yeremiya 6:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kodi iwo anachita manyazi chifukwa chochita zinthu zonyansazi?+ Iwo sanachite manyazi ngakhale pang’ono, komanso sadziwa n’komwe kuchita manyazi.+ Choncho iwo adzagwa pamodzi ndi anthu amene akugwa.+ Pamene ndidzakhala ndikuwaimba mlandu adzapunthwa,” watero Yehova.

  • Yuda 18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 mmene anali kukuuzani kuti: “M’masiku otsiriza kudzakhala onyodola, otsatira zilakolako zawo pa zinthu zonyoza Mulungu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena