Miyambo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 yothandiza munthu kupeza nzeru+ ndi malangizo,*+ kuti amvetse mawu ozama,+ Miyambo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nzeru zikalowa mumtima mwako,+ ndipo kudziwa zinthu kukakhala kosangalatsa m’moyo wako,+ Miyambo 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amakondwera ndi uchitsiru,+ koma munthu wozindikira ndi amene amayenda panjira yabwino.+
21 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amakondwera ndi uchitsiru,+ koma munthu wozindikira ndi amene amayenda panjira yabwino.+