Miyambo 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kwa wopusa, kusonyeza khalidwe lotayirira kuli ngati masewera,+ koma nzeru zimakhala ndi munthu wozindikira.+ Miyambo 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndi mmenenso alili munthu amene amapusitsa mnzake, n’kunena kuti: “Inetu ndimangochita zocheza.”+ Mlaliki 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtima wa anthu anzeru umakhala m’nyumba yamaliro,+ koma mtima wa anthu opusa umakhala m’nyumba yachisangalalo.+
23 Kwa wopusa, kusonyeza khalidwe lotayirira kuli ngati masewera,+ koma nzeru zimakhala ndi munthu wozindikira.+
4 Mtima wa anthu anzeru umakhala m’nyumba yamaliro,+ koma mtima wa anthu opusa umakhala m’nyumba yachisangalalo.+