Miyambo 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kwa wopusa, kusonyeza khalidwe lotayirira kuli ngati masewera,+ koma nzeru zimakhala ndi munthu wozindikira.+ Miyambo 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amakondwera ndi uchitsiru,+ koma munthu wozindikira ndi amene amayenda panjira yabwino.+
23 Kwa wopusa, kusonyeza khalidwe lotayirira kuli ngati masewera,+ koma nzeru zimakhala ndi munthu wozindikira.+
21 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amakondwera ndi uchitsiru,+ koma munthu wozindikira ndi amene amayenda panjira yabwino.+