Miyambo 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu opusa akapalamula mlandu amangoseka,+ koma pakati pa anthu owongoka mtima pali mgwirizano.+ Miyambo 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndi mmenenso alili munthu amene amapusitsa mnzake, n’kunena kuti: “Inetu ndimangochita zocheza.”+