Nehemiya 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa tsiku la 24 la mwezi umenewu+ ana a Isiraeli anasonkhana pamodzi. Iwo anali kusala kudya+ atavala ziguduli*+ ndiponso atadzithira dothi+ kumutu. Danieli 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinayang’ana+ kwa Yehova Mulungu woona kuti ndimufunefune mwa kupemphera,+ kumuchonderera, kusala kudya, kuvala ziguduli* ndi kudzithira phulusa.+
9 Pa tsiku la 24 la mwezi umenewu+ ana a Isiraeli anasonkhana pamodzi. Iwo anali kusala kudya+ atavala ziguduli*+ ndiponso atadzithira dothi+ kumutu.
3 Ndinayang’ana+ kwa Yehova Mulungu woona kuti ndimufunefune mwa kupemphera,+ kumuchonderera, kusala kudya, kuvala ziguduli* ndi kudzithira phulusa.+