Salimo 94:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zindikirani anthu opanda nzeru inu.+Ndipo opusa inu, mudzakhala liti ozindikira?+ Miyambo 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu wanzeru akakhala pa mlandu ndi chitsiru, chitsirucho chimangochita phokoso n’kumaseka, ndipo munthu wanzeruyo sapeza mpumulo.+
9 Munthu wanzeru akakhala pa mlandu ndi chitsiru, chitsirucho chimangochita phokoso n’kumaseka, ndipo munthu wanzeruyo sapeza mpumulo.+