Salimo 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti amaona kuti ngakhale anthu anzeru amafa,+Wopusa ndi wopanda nzeru, onsewo amawonongeka,+Ndipo chuma chawo amasiyira anthu ena.+ Salimo 73:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndinakhala wopanda nzeru ndipo sindinadziwe kanthu.+Ndinakhala ngati nyama yakuthengo pamaso panu.+ Salimo 92:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthu wopanda nzeru sangadziwe zimenezi,+Ndipo munthu wopusa sangazimvetse.+ Miyambo 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wokonda malangizo* amakondanso kudziwa zinthu,+ koma wodana ndi chidzudzulo ndi wopanda nzeru.+
10 Pakuti amaona kuti ngakhale anthu anzeru amafa,+Wopusa ndi wopanda nzeru, onsewo amawonongeka,+Ndipo chuma chawo amasiyira anthu ena.+
22 Ndinakhala wopanda nzeru ndipo sindinadziwe kanthu.+Ndinakhala ngati nyama yakuthengo pamaso panu.+