Miyambo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwana wanga, usakane malangizo* a Yehova+ ndipo usanyansidwe ndi kudzudzula kwake,+ Miyambo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gwira malangizo,+ usawataye.+ Uwasunge bwino chifukwa iwo ndiwo moyo wako.+ Miyambo 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Bweretsa mtima wako kuti umve malangizo, ndi khutu lako kuti limve mawu a munthu wodziwa zinthu.+