Deuteronomo 32:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Pakuti amenewa si mawu opanda pake kwa inu,+ chifukwa mawu amenewa ndiwo moyo wanu.+ Mwa kutsatira mawu amenewa mudzatalikitsa masiku anu panthaka imene mukupita kukaitenga kukhala yanu, mutawoloka Yorodano.”+ Miyambo 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ndipo zidzatanthauza moyo kwa iwe+ komanso zidzakhala chokongoletsa m’khosi mwako.+
47 Pakuti amenewa si mawu opanda pake kwa inu,+ chifukwa mawu amenewa ndiwo moyo wanu.+ Mwa kutsatira mawu amenewa mudzatalikitsa masiku anu panthaka imene mukupita kukaitenga kukhala yanu, mutawoloka Yorodano.”+