Miyambo 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti izo ndi moyo kwa amene amazipeza+ ndiponso ndi thanzi labwino kwa thupi lawo lonse.+