Miyambo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Bambo anga anali kundilangiza+ kuti: “Mtima wako+ ugwire mwamphamvu mawu anga.+ Sunga malamulo anga kuti upitirize kukhala ndi moyo.+ 1 Timoteyo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti kuchita masewera olimbitsa thupi n’kopindulitsa pang’ono, koma kukhala wodzipereka kwa Mulungu+ n’kopindulitsa m’zonse,+ chifukwa kumakhudza lonjezo la moyo uno ndi moyo umene ukubwerawo.+
4 Bambo anga anali kundilangiza+ kuti: “Mtima wako+ ugwire mwamphamvu mawu anga.+ Sunga malamulo anga kuti upitirize kukhala ndi moyo.+
8 Pakuti kuchita masewera olimbitsa thupi n’kopindulitsa pang’ono, koma kukhala wodzipereka kwa Mulungu+ n’kopindulitsa m’zonse,+ chifukwa kumakhudza lonjezo la moyo uno ndi moyo umene ukubwerawo.+