Miyambo 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Landirani malangizo* anga osati siliva, ndiponso kudziwa zinthu m’malo mwa golide wabwino kwambiri.+ Miyambo 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mverani malangizo kuti mukhale anzeru,+ ndipo musawanyalanyaze.+ Miyambo 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Gula choonadi+ ndipo usachigulitse. Gula nzeru, malangizo ndi kumvetsa zinthu.+ Aheberi 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+
10 Landirani malangizo* anga osati siliva, ndiponso kudziwa zinthu m’malo mwa golide wabwino kwambiri.+
6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+