Miyambo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwana wanga, usakane malangizo* a Yehova+ ndipo usanyansidwe ndi kudzudzula kwake,+ Miyambo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gwira malangizo,+ usawataye.+ Uwasunge bwino chifukwa iwo ndiwo moyo wako.+ Aheberi 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kupirira kumene mukupiriraku,+ mukupirira kuti chikhale chilango chanu. Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samulanga?+
7 Kupirira kumene mukupiriraku,+ mukupirira kuti chikhale chilango chanu. Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samulanga?+