Yohane 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mudzadziwa choonadi,+ ndipo choonadi chidzakumasulani.”+ Afilipi 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma zinthu zimene zinali zaphindu kwa ine, zimenezo ndaziona kukhala zopanda phindu chifukwa cha Khristu.+
7 Koma zinthu zimene zinali zaphindu kwa ine, zimenezo ndaziona kukhala zopanda phindu chifukwa cha Khristu.+