Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 119:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  45 Ndidzayenda uku ndi uku m’malo otakasuka,+

      Chifukwa ndaphunzira malamulo anu ndi kuwasunga.+

  • Luka 4:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Mzimu wa Yehova+ uli pa ine, chifukwa iye anandidzoza kuti ndilengeze uthenga wabwino kwa osauka. Anandituma kudzalalikira za kumasulidwa kwa ogwidwa ukapolo, ndi zoti akhungu ayambe kuona. Anandituma kudzamasula oponderezedwa kuti akhale mfulu,+

  • Aroma 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Uchimo usakhale mbuye kwa inu, chifukwa simuli pansi pa chilamulo+ koma pansi pa kukoma mtima kwakukulu.+

  • Aroma 6:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Koma tsopano chifukwa munamasulidwa ku uchimo ndipo munakhala akapolo a Mulungu,+ mukukhala ndi zipatso+ za chiyero, ndipo pa mapeto pake mudzakhala ndi moyo wosatha.+

  • Aheberi 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Anachitanso zimenezi kuti amasule+ onse amene poopa imfa,+ anali mu ukapolo moyo wawo wonse.+

  • Yakobo 1:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Koma woyang’anitsitsa m’lamulo langwiro+ limene limabweretsa ufulu, amene amalimbikira kutero, adzakhala wosangalala+ polichita chifukwa chakuti sali wongomva n’kuiwala, koma wochita.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena