Salimo 73:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndinakhala wopanda nzeru ndipo sindinadziwe kanthu.+Ndinakhala ngati nyama yakuthengo pamaso panu.+ Salimo 94:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zindikirani anthu opanda nzeru inu.+Ndipo opusa inu, mudzakhala liti ozindikira?+ Danieli 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu ambiri adzadzitsuka,+ adzadziyeretsa+ ndipo adzayengedwa.+ Anthu oipa adzachita zinthu zoipa+ ndipo palibe munthu woipa aliyense amene adzamvetsetse mawu amenewa,+ koma anthu ozindikira adzawamvetsetsa.+
22 Ndinakhala wopanda nzeru ndipo sindinadziwe kanthu.+Ndinakhala ngati nyama yakuthengo pamaso panu.+
10 Anthu ambiri adzadzitsuka,+ adzadziyeretsa+ ndipo adzayengedwa.+ Anthu oipa adzachita zinthu zoipa+ ndipo palibe munthu woipa aliyense amene adzamvetsetse mawu amenewa,+ koma anthu ozindikira adzawamvetsetsa.+