Salimo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu wopusa* amanena mumtima mwake kuti: “Kulibe Yehova.”+ Zochita za anthu amenewa ndi zoipa komanso zonyansa,Ndipo palibe amene akuchita zabwino.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:1 Nsanja ya Olonda,10/1/1997, ptsa. 6-7
14 Munthu wopusa* amanena mumtima mwake kuti: “Kulibe Yehova.”+ Zochita za anthu amenewa ndi zoipa komanso zonyansa,Ndipo palibe amene akuchita zabwino.+