Salimo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:“Kulibe Yehova.”+Anthu oterewa amachita zoipa,+ ndipo amachita zinthu zonyansa.Palibe amene akuchita zabwino.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:1 Nsanja ya Olonda,10/1/1997, ptsa. 6-7
14 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:“Kulibe Yehova.”+Anthu oterewa amachita zoipa,+ ndipo amachita zinthu zonyansa.Palibe amene akuchita zabwino.+