Miyambo 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Milomo ya wolungama imaweta anthu ambiri,+ koma zitsiru zimafa chifukwa chopanda nzeru mumtima.+ Miyambo 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mawu okoma ali ngati chisa cha uchi.+ Amakhala okoma kwa munthu ndipo amachiritsa mafupa.+