Miyambo 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nkhawa mumtima mwa munthu ndi imene imauweramitsa,+ koma mawu abwino ndi amene amausangalatsa.+ Miyambo 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mtima wachimwemwe umapangitsa nkhope kusangalala,+ koma chifukwa cha kupweteka kwa mtima munthu sasangalala.+
13 Mtima wachimwemwe umapangitsa nkhope kusangalala,+ koma chifukwa cha kupweteka kwa mtima munthu sasangalala.+