Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 13:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chinthu chimene unali kuyembekeza chikalephereka, chimadwalitsa mtima.+ Koma chomwe unali kufuna chikachitika, chimakhala ngati mtengo wa moyo.+

  • Miyambo 16:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mawu okoma ali ngati chisa cha uchi.+ Amakhala okoma kwa munthu ndipo amachiritsa mafupa.+

  • Yesaya 50:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wandipatsa lilime la anthu ophunzitsidwa bwino+ kuti ndidziwe mmene ndingamuyankhire munthu wotopa.+ Iye amandidzutsa m’mawa uliwonse. Amandidzutsa kuti makutu anga amve ngati anthu ophunzitsidwa bwino.+

  • Zekariya 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova anayankha mngelo amene anali kulankhula ndi ine uja. Anamuyankha ndi mawu abwino ndiponso olimbikitsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena