Ekisodo 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Yehova anamuuza kuti: “Anapatsa munthu pakamwa ndani, kapena ndani amapanga munthu wosalankhula, wogontha, woona kapena wakhungu? Kodi si ine, Yehova?+ Yeremiya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Yehova anatambasula dzanja lake ndi kukhudza pakamwa panga.+ Ndiyeno Yehova anandiuza kuti: “Ndaika mawu anga m’kamwa mwako.+ Yohane 7:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Alondawo anayankha kuti: “Palibe munthu amene analankhulapo ngati iyeyu n’kale lonse.”+
11 Pamenepo Yehova anamuuza kuti: “Anapatsa munthu pakamwa ndani, kapena ndani amapanga munthu wosalankhula, wogontha, woona kapena wakhungu? Kodi si ine, Yehova?+
9 Pamenepo Yehova anatambasula dzanja lake ndi kukhudza pakamwa panga.+ Ndiyeno Yehova anandiuza kuti: “Ndaika mawu anga m’kamwa mwako.+