Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 94:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Kodi amene anakupatsani makutu, sangamve?+

      Kapena amene anapanga maso, sangaone?+

  • Yesaya 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ukachititse anthu awa kuumitsa mtima wawo,+ ndipo ukachititse makutu awo kuti asamamve.+ Ukamate maso awo kuti asamaone ndi maso awowo, ndiponso kuti asamamve ndi makutu awo, komanso kuti mtima wawo usamvetsetse zinthu, kuti angatembenuke n’kuchira.”+

  • Luka 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Imva tsopano! Udzakhala chete,+ osatha kulankhula mpaka tsiku limene zimenezi zidzachitike. Izi zidzachitika chifukwa sunakhulupirire mawu anga amene adzakwaniritsidwe pa nthawi yake yoikidwiratu.”

  • Machitidwe 13:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano tamvera! Dzanja la Yehova lili pa iwe, ndipo ukhala wakhungu. Kwa kanthawi, suthanso kuona kuwala kwa dzuwa.” Nthawi yomweyo nkhungu yamphamvu ndi mdima wandiweyani zinamugwera, ndipo anafufuza uku ndi uku kufuna anthu oti amugwire dzanja ndi kumutsogolera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena