Ezekieli 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndidzachititsa lilime lako kumatirira kumwamba m’kamwa mwako,+ ndipo sudzathanso kulankhula.+ Sudzakhalanso munthu wowadzudzula,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka.+ Ezekieli 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pa tsiku limenelo udzatsegula pakamwa pako n’kulankhula ndi wothawayo+ ndipo sudzakhalanso chete.+ Choncho iwe udzakhala chizindikiro kwa iwo cholosera zam’tsogolo,+ ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”+
26 Ndidzachititsa lilime lako kumatirira kumwamba m’kamwa mwako,+ ndipo sudzathanso kulankhula.+ Sudzakhalanso munthu wowadzudzula,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka.+
27 Pa tsiku limenelo udzatsegula pakamwa pako n’kulankhula ndi wothawayo+ ndipo sudzakhalanso chete.+ Choncho iwe udzakhala chizindikiro kwa iwo cholosera zam’tsogolo,+ ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”+