Ezekieli 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndidzachititsa lilime lako kumatirira kumwamba m’kamwa mwako,+ ndipo sudzathanso kulankhula.+ Sudzakhalanso munthu wowadzudzula,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka.+ Ezekieli 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano madzulo, munthu wopulumuka uja asanafike, dzanja la Yehova linandikhudza.+ Ndipo Mulungu anatsegula pakamwa panga, wopulumuka uja asanafike m’mawa. Pakamwa panga panatseguka ndipo ndinayambanso kulankhula.+ Luka 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Imva tsopano! Udzakhala chete,+ osatha kulankhula mpaka tsiku limene zimenezi zidzachitike. Izi zidzachitika chifukwa sunakhulupirire mawu anga amene adzakwaniritsidwe pa nthawi yake yoikidwiratu.”
26 Ndidzachititsa lilime lako kumatirira kumwamba m’kamwa mwako,+ ndipo sudzathanso kulankhula.+ Sudzakhalanso munthu wowadzudzula,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka.+
22 Tsopano madzulo, munthu wopulumuka uja asanafike, dzanja la Yehova linandikhudza.+ Ndipo Mulungu anatsegula pakamwa panga, wopulumuka uja asanafike m’mawa. Pakamwa panga panatseguka ndipo ndinayambanso kulankhula.+
20 Imva tsopano! Udzakhala chete,+ osatha kulankhula mpaka tsiku limene zimenezi zidzachitike. Izi zidzachitika chifukwa sunakhulupirire mawu anga amene adzakwaniritsidwe pa nthawi yake yoikidwiratu.”