Ezekieli 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pa tsiku limenelo udzatsegula pakamwa pako n’kulankhula ndi wothawayo+ ndipo sudzakhalanso chete.+ Choncho iwe udzakhala chizindikiro kwa iwo cholosera zam’tsogolo,+ ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”+ Luka 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma pamene anatuluka sanathenso kulankhula nawo. Pamenepo iwo anazindikira kuti waona masomphenya+ a chinachake m’nyumba yopatulikayo. Choncho anayamba kulankhula nawo ndi manja okhaokha, osathanso kutulutsa mawu.
27 Pa tsiku limenelo udzatsegula pakamwa pako n’kulankhula ndi wothawayo+ ndipo sudzakhalanso chete.+ Choncho iwe udzakhala chizindikiro kwa iwo cholosera zam’tsogolo,+ ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”+
22 Koma pamene anatuluka sanathenso kulankhula nawo. Pamenepo iwo anazindikira kuti waona masomphenya+ a chinachake m’nyumba yopatulikayo. Choncho anayamba kulankhula nawo ndi manja okhaokha, osathanso kutulutsa mawu.