Ekisodo 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ine ndidzamusiya Farao kuti aumitse mtima wake,+ ndipo ndidzachita zizindikiro ndi zozizwitsa zochuluka m’dziko la Iguputo.+ 1 Samueli 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso, mukuumitsiranji mitima yanu mmene Aiguputo ndi Farao anaumitsira mitima yawo?+ Si paja Mulungu atangowakhaulitsa+ analola Aisiraeli kupita, ndipo iwo anapitadi?+ Ezekieli 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma a nyumba ya Isiraeli sakafuna kukumvera, chifukwa iwo safuna kundimvera.+ Pakuti anthu onse a nyumba ya Isiraeli ndi amakani ndi osamva.+ 2 Akorinto 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kwa amene akupita kukawonongedwawo ndife fungo lochokera ku imfa kupita ku imfa,+ koma kwa amene akupita kukapulumukawo ndife fungo lochokera ku moyo kupita ku moyo. Ndipo ndani ali woyenerera kugwira ntchito imeneyi?+
3 Koma ine ndidzamusiya Farao kuti aumitse mtima wake,+ ndipo ndidzachita zizindikiro ndi zozizwitsa zochuluka m’dziko la Iguputo.+
6 Komanso, mukuumitsiranji mitima yanu mmene Aiguputo ndi Farao anaumitsira mitima yawo?+ Si paja Mulungu atangowakhaulitsa+ analola Aisiraeli kupita, ndipo iwo anapitadi?+
7 Koma a nyumba ya Isiraeli sakafuna kukumvera, chifukwa iwo safuna kundimvera.+ Pakuti anthu onse a nyumba ya Isiraeli ndi amakani ndi osamva.+
16 Kwa amene akupita kukawonongedwawo ndife fungo lochokera ku imfa kupita ku imfa,+ koma kwa amene akupita kukapulumukawo ndife fungo lochokera ku moyo kupita ku moyo. Ndipo ndani ali woyenerera kugwira ntchito imeneyi?+