Yohane 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukanakhala mbali ya dziko, dziko likanakukondani monga mbali yake.+ Koma popeza simuli mbali ya dzikoli,+ koma ine ndinakusankhani kuchokera m’dziko, pa chifukwa chimenechi dziko likudana nanu.+ 2 Akorinto 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano ngati uthenga wabwino umene tikulengeza uli wophimbika, ndi wophimbika pakati pa anthu amene akupita kukawonongedwa.+ 1 Petulo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 komanso “mwala wopunthwitsa ndi thanthwe lokhumudwitsa.”+ Anthu amenewa akupunthwa chifukwa samvera mawu, ndipo anaikidwiratu kale kuti adzatero.+
19 Mukanakhala mbali ya dziko, dziko likanakukondani monga mbali yake.+ Koma popeza simuli mbali ya dzikoli,+ koma ine ndinakusankhani kuchokera m’dziko, pa chifukwa chimenechi dziko likudana nanu.+
3 Tsopano ngati uthenga wabwino umene tikulengeza uli wophimbika, ndi wophimbika pakati pa anthu amene akupita kukawonongedwa.+
8 komanso “mwala wopunthwitsa ndi thanthwe lokhumudwitsa.”+ Anthu amenewa akupunthwa chifukwa samvera mawu, ndipo anaikidwiratu kale kuti adzatero.+