Luka 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Ndinu odala anthu akamadana nanu,+ kukusalani, kukunyozani ndi kukana+ dzina lanu n’kumanena kuti ndi loipa, chifukwa cha Mwana wa munthu. 1 Petulo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa chakuti simukupitiriza kuthamanga nawo limodzi m’chithaphwi cha makhalidwe oipa,+ anthu a m’dzikoli sakumvetsa, choncho amakunyozani.+
22 “Ndinu odala anthu akamadana nanu,+ kukusalani, kukunyozani ndi kukana+ dzina lanu n’kumanena kuti ndi loipa, chifukwa cha Mwana wa munthu.
4 Chifukwa chakuti simukupitiriza kuthamanga nawo limodzi m’chithaphwi cha makhalidwe oipa,+ anthu a m’dzikoli sakumvetsa, choncho amakunyozani.+