Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 21:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamenepo Mulungu anamva mawu a mnyamatayo,+ ndipo mngelo wa Mulungu analankhula ndi Hagara kuchokera kumwamba+ kuti: “Kodi watani Hagara? Usaope, Mulungu wamva mawu a mnyamatayo pomwe wagonapo.

  • Ekisodo 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo Yehova anamuuza kuti: “Anapatsa munthu pakamwa ndani, kapena ndani amapanga munthu wosalankhula, wogontha, woona kapena wakhungu? Kodi si ine, Yehova?+

  • Salimo 55:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mulungu amene wakhala pampando wachifumu kuyambira kalekale,+

      Adzandimvera ndipo adzawayankha,+ [Seʹlah.]

      Anthu osafuna kusintha makhalidwe awo oipa,+

      Ndiponso amene saopa Mulungu.+

  • Salimo 69:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Pakuti Yehova akumvetsera osauka,+

      Ndipo sadzanyoza anthu ake amene ali m’ndende.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena