Salimo 69:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pakuti Yehova akumvetsera osauka,+Ndipo sadzanyoza anthu ake amene ali m’ndende.+ Salimo 143:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Adani anga muwakhalitse chete monga mwa kukoma mtima kwanu kosatha.+Ndipo muwononge onse ondichitira zoipa,+Pakuti ine ndine mtumiki wanu.+
12 Adani anga muwakhalitse chete monga mwa kukoma mtima kwanu kosatha.+Ndipo muwononge onse ondichitira zoipa,+Pakuti ine ndine mtumiki wanu.+