Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 16:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mngelo wa Yehovayo anapitiriza kulankhula ndi mkaziyo kuti: “Taona, panopo uli ndi pakati, ndipo udzabereka mwana wamwamuna. Mwanayo udzamutche Isimaeli,+ pakuti Yehova wamva kulira kwako.+

  • Salimo 22:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pakuti iye sananyoze,+

      Kapena kunyansidwa ndi nsautso ya munthu wosautsidwa.+

      Ndipo sanam’bisire nkhope yake.+

      Pamene anamulirira kuti amuthandize, iye anamva.+

  • Salimo 68:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Tate wa ana amasiye* ndi woweruzira akazi amasiye milandu,+

      Ndi Mulungu amene amakhala m’malo ake oyera.+

  • Salimo 146:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Yehova amayang’anira alendo okhala m’dziko la eni.+

      Amathandiza mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.+

      Koma njira+ ya anthu oipa amaichititsa kukhala yovuta kuyendamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena