Salimo 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chifukwa iye sananyoze kapena kunyansidwa ndi kuvutika kwa munthu woponderezedwa.+Sanabise nkhope yake kwa iye.+ Pamene anamulirira kuti amuthandize, iye anamva.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:24 Nsanja ya Olonda,8/1/2005, ptsa. 26-27
24 Chifukwa iye sananyoze kapena kunyansidwa ndi kuvutika kwa munthu woponderezedwa.+Sanabise nkhope yake kwa iye.+ Pamene anamulirira kuti amuthandize, iye anamva.+