Salimo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+ Miyambo 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Khutu lakumva ndiponso diso loona, zonsezi anazipanga ndi Yehova.+