Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo Yehova anamuuza kuti: “Anapatsa munthu pakamwa ndani, kapena ndani amapanga munthu wosalankhula, wogontha, woona kapena wakhungu? Kodi si ine, Yehova?+

  • Salimo 94:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Kodi amene anakupatsani makutu, sangamve?+

      Kapena amene anapanga maso, sangaone?+

  • Machitidwe 26:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ukatsegule maso awo,+ kuwachotsa mu mdima+ ndi kuwatembenuzira ku kuwala.+ Kuwachotsa m’manja mwa Satana+ ndi kuwatembenuzira kwa Mulungu, kuti machimo awo akhululukidwe+ ndi kukalandira cholowa+ pamodzi ndi oyeretsedwa,+ mwa chikhulupiriro chawo mwa ine.’

  • Aefeso 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Popeza maso+ a mtima wanu aunikiridwa,+ ndikukutchulanibe m’mapemphero anga kutinso mudziwe chiyembekezo+ chimene anakuitanirani, chuma chaulemerero+ chimene wasungira oyera monga cholowa,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena