Yesaya 42:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 kuti ukatsegule maso a akhungu,+ ukatulutse mkaidi m’ndende ya mdima+ ndiponso kuti ukatulutse m’ndende anthu amene ali mu mdima.+ Akolose 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anatilanditsa ku ulamuliro+ wa mdima, n’kutisamutsira+ mu ufumu+ wa Mwana wake wokondedwa.+
7 kuti ukatsegule maso a akhungu,+ ukatulutse mkaidi m’ndende ya mdima+ ndiponso kuti ukatulutse m’ndende anthu amene ali mu mdima.+