Luka 22:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Tsiku ndi tsiku ndinali nanu m’kachisi+ koma simunandigwire.+ Koma ino tsopano ndi nthawi yanu+ komanso nthawi ya ulamuliro+ wa mdima.”+ Aefeso 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munali kuyenda m’zimenezo mogwirizana ndi nthawi*+ za m’dzikoli, momveranso wolamulira+ wa mpweya umene umalamulira zochita za anthu. Mpweya umenewu, kapena kuti kaganizidwe kameneka,+ tsopano kakugwira ntchito mwa ana a kusamvera.+
53 Tsiku ndi tsiku ndinali nanu m’kachisi+ koma simunandigwire.+ Koma ino tsopano ndi nthawi yanu+ komanso nthawi ya ulamuliro+ wa mdima.”+
2 Munali kuyenda m’zimenezo mogwirizana ndi nthawi*+ za m’dzikoli, momveranso wolamulira+ wa mpweya umene umalamulira zochita za anthu. Mpweya umenewu, kapena kuti kaganizidwe kameneka,+ tsopano kakugwira ntchito mwa ana a kusamvera.+