Aroma 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musamatengere+ nzeru za nthawi* ino, koma sandulikani mwa kusintha maganizo anu,+ kuti muzindikire+ chimene chili chifuniro+ cha Mulungu, chabwino, chovomerezeka ndi changwiro. Aefeso 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho, ndikunena izi ndi kuzichitira umboni mwa Ambuye, kuti musamayendenso monga mmene anthu a mitundu ina+ amayendera, potsatira maganizo awo opanda pake.+
2 Musamatengere+ nzeru za nthawi* ino, koma sandulikani mwa kusintha maganizo anu,+ kuti muzindikire+ chimene chili chifuniro+ cha Mulungu, chabwino, chovomerezeka ndi changwiro.
17 Choncho, ndikunena izi ndi kuzichitira umboni mwa Ambuye, kuti musamayendenso monga mmene anthu a mitundu ina+ amayendera, potsatira maganizo awo opanda pake.+