Machitidwe 20:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma tsopano ndikukuperekani kwa Mulungu+ ndi ku mawu a kukoma mtima kwake kwakukulu. Mawu amenewo angakulimbikitseni+ ndi kukupatsani cholowa pakati pa oyeretsedwa onse.+
32 Koma tsopano ndikukuperekani kwa Mulungu+ ndi ku mawu a kukoma mtima kwake kwakukulu. Mawu amenewo angakulimbikitseni+ ndi kukupatsani cholowa pakati pa oyeretsedwa onse.+