Miyambo 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Munthu amasangalala ndi yankho lochokera pakamwa pake,+ ndipo mawu onenedwa pa nthawi yoyenera ndi abwino kwambiri.+ Mateyu 13:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Atafika m’dera lakwawo+ anayamba kuwaphunzitsa m’sunagoge wawo,+ moti anthu anadabwa ndipo anali kunena kuti: “Kodi munthu ameneyu, nzeru ndi ntchito zamphamvu zoterezi anazitenga kuti?
23 Munthu amasangalala ndi yankho lochokera pakamwa pake,+ ndipo mawu onenedwa pa nthawi yoyenera ndi abwino kwambiri.+
54 Atafika m’dera lakwawo+ anayamba kuwaphunzitsa m’sunagoge wawo,+ moti anthu anadabwa ndipo anali kunena kuti: “Kodi munthu ameneyu, nzeru ndi ntchito zamphamvu zoterezi anazitenga kuti?