Miyambo 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu amakhutitsidwa ndi zabwino kuchokera ku zipatso za pakamwa pake,+ ndipo zochita za manja a munthu, zidzabwerera kwa iye.+ Miyambo 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Milomo yolungama imasangalatsa mfumu yaikulu,+ ndipo mfumuyo imakonda munthu wolankhula zinthu zowongoka.+ Aefeso 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mawu alionse owola asatuluke pakamwa panu,+ koma alionse olimbikitsa monga mmene kungafunikire, kuti asangalatse owamva.+
14 Munthu amakhutitsidwa ndi zabwino kuchokera ku zipatso za pakamwa pake,+ ndipo zochita za manja a munthu, zidzabwerera kwa iye.+
13 Milomo yolungama imasangalatsa mfumu yaikulu,+ ndipo mfumuyo imakonda munthu wolankhula zinthu zowongoka.+
29 Mawu alionse owola asatuluke pakamwa panu,+ koma alionse olimbikitsa monga mmene kungafunikire, kuti asangalatse owamva.+