16 Kodi simukudziwa kuti ngati mudziperekabe kwa winawake monga akapolo kuti muzimumvera, mumakhala akapolo ake chifukwa chakuti mumamumvera,+ kaya mukhale akapolo a uchimo+ umene umatsogolera ku imfa,+ kapena mukhale akapolo a kumvera+ kumene kumatsogolera ku chilungamo?+