Deuteronomo 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 (Mose anatipatsa chilamulo,+Chimene mpingo wa Yakobo uli nacho monga chawo.)+ Salimo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma amakondwera ndi chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kusinkhasinkha chilamulo chake usana ndi usiku.+ Salimo 78:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 78 Inu anthu anga, mvetserani chilamulo changa.+Tcherani khutu ku mawu a pakamwa panga.+
2 Koma amakondwera ndi chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kusinkhasinkha chilamulo chake usana ndi usiku.+