Ezekieli 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, idya chimene chili pamaso pakochi. Idya mpukutuwu,+ kenako upite kukalankhula ndi nyumba ya Isiraeli.” Chivumbulutso 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero ndinatenga mpukutu waung’onowo m’dzanja la mngeloyo n’kuudya.+ M’kamwa mwanga, unali wozuna ngati uchi,+ koma nditaudya, unandipweteketsa m’mimba.
3 Iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, idya chimene chili pamaso pakochi. Idya mpukutuwu,+ kenako upite kukalankhula ndi nyumba ya Isiraeli.”
10 Chotero ndinatenga mpukutu waung’onowo m’dzanja la mngeloyo n’kuudya.+ M’kamwa mwanga, unali wozuna ngati uchi,+ koma nditaudya, unandipweteketsa m’mimba.