Chivumbulutso 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndinatengadi mpukutu waungʼonowo mʼdzanja la mngeloyo nʼkuudya.+ Mʼkamwa mwanga unkakoma ngati uchi,+ koma nditaudya mʼmimba mwanga munayamba kupweteka. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:10 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 158-160 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, tsa. 1310/15/1988, tsa. 14
10 Ndinatengadi mpukutu waungʼonowo mʼdzanja la mngeloyo nʼkuudya.+ Mʼkamwa mwanga unkakoma ngati uchi,+ koma nditaudya mʼmimba mwanga munayamba kupweteka.